Leviticus 20:22 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Nchifukwa chake muzisunga malamulo anga, ndipo muzichita zonse zimene ndimakulamulani ndi kuzitsata, kuti dziko limene mukupita kuti mukakhalemolo lingakudeni.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Potero muzisunga malemba anga onse, ndi maweruzo anga onse, kuwachita; lingakusanzeni inu dziko limene ndipita nanuko, kuti mukhale m'mwemo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“ ‘Nʼchifukwa chake muzisunga malangizo anga onse ndi malamulo anga ndipo muwatsatire kuti ku dziko limene Ine ndikupita nanu kuti mukakhalemo lisakakusanzeni.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Potero muzisunga malemba anga onse, ndi maweruzo anga onse, kuwacita; lingakusanzeni inu dziko limene ndipita nanuko, kuti mukhale m'mwemo.