Leviticus 20:4 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Anthu am'dzikomo akachita ngati sakumuwona munthuyo, pamene akupereka mmodzi mwa ana ake kwa Moleki, namleka osamupha,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo ngati anthu a m'dzikomo akambisa munthuyo pang'ono ponse, pamene apereka a mbeu zake kwa Moleki, kuti asamuphe;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ngati anthu a mʼderalo achita ngati sakumuona munthuyo pamene akupereka mwana wake kwa Moleki ndi kusamupha,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo ngati anthu a m'dzikomo akambisa munthuyo pang'ono ponse, pamene apereka a mbeu zace kwa Moleke, kuti asamuphe;