Leviticus 21:11 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Asakaloŵe kumene kuli munthu wakufa aliyense ndi kudziipitsa, ngakhale mtembo wa bambo wake kapena wa mai wake.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Asafike kuli mtembo; asadzidetse chifukwa cha atate wake, kapena mai wake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Asalowe mʼnyumba mmene muli munthu wakufa ngakhale womwalirayo ndi amayi ake kapena abambo ake.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Asafike kuli mtembo; asadzidetse cifukwa ca atate wace, kapena mai wace.