Leviticus 21:18 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Munthu aliyense wachilema sayenera kusendera pafupi, monga munthu wakhungu kapena wopunduka miyendo, munthu wopunduka nkhope kapena wokhala ndi chiwalo china chachitali dziŵi,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pakuti munthu aliyense wokhala nacho chilema, asayandikize; wakhungu, kapena wotsimphina, kapena wopunduka mphuno, kapena wamkulu chiwalo,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Munthu aliyense wachilema motere: munthu wakhungu kapena wolumala miyendo, munthu wolumala nkhope kapena waziwalo zambiri,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakuti munthu ali yense wokhala naco cirema, asayandikize; wakhungu, kapena wotsimphina, kapena wopunduka mph uno, kapena wamkuru ciwalo,