Leviticus 21:2 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma angathe kukhudza mai wake, bambo wake, mwana wake wamwamuna, mwana wake wamkazi,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
koma chifukwa cha abale ake enieni ndiwo, mai wake, ndi atate wake, ndi mwana wake wamwamuna, ndi mwana wake wamkazi, ndi mbale wake;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma akhoza kukhudza thupi lakufa la amayi ake, abambo ake, mwana wake wamwamuna, mwana wake wamkazi, mchimwene wake,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
koma cifukwa ca abale ace eni eni ndiwo, mai wace, ndi atate wace, ndi mwana wace wamwamuna, ndi mwana wace wamkazi, ndi mbale wace;