Leviticus 21:20 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
munthu wanundu kapena kafupidolo, munthu wa maso opunduka, munthu wa nthenda yonyerenyesa, kapena wamphere, kapenanso wotswanyika mavalo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
kapena wowerama, kapena wamfupi msinkhu, kapena wopunduka diso, kapena munthu wamphere, kapena wachipere, kapena wopunduka kumoto.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
kapena munthu wokhota msana kapena wamfupi kwambiri, kapena wolumala maso, munthu wa nthenda yonyerenyetsa, kapena wamphere, kapenanso wophwanyika mavalo, sayenera kusendera pafupi.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
kapena wowerama, kapena wamfupi msinkhu, kapena wopunduka diso, kapena munthu wamphere, kapena wacipere, kapena wopunduka kumoto.