Leviticus 21:4 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Wansembe asadziipitse pa imfa ya munthu amene wakwatira naye ku banja limodzi.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Akakhala mwini banja pakati pa anthu a mtundu wake, asadzidetse, ndi kudziipsa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma wansembe asadzidetse chifukwa cha anthu amene ali nawo pa ubale obwera chifukwa cha ukwati.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Akakhala mwini banja pakati pa anthu a mtundu wace, asadzidetse, ndi kudziipsa,