Leviticus 21:8 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Akhale munthu woyera kwa inu, chifukwa amapereka chakudya cha Mulungu wanu. Akhale munthu woyera kwa inu, chifukwa Ine Chauta amene ndimakuyeretsani, ndine woyera.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Chifukwa chake umpatule; popeza amapereka mkate wa Mulungu wako; umuyese wopatulika; pakuti Ine Yehova wakupatula iwe, ndine woyera,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iwo akhale oyera chifukwa amapereka nsembe kwa Mulungu wanu. Muziwaona kuti ndi oyera, popeza Ine Yehova amene ndimawayeretsa ndine woyera, nawonso akhale oyera.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Cifukwa cace umpatule; popeza amapereka mkate wa Mulungu wako; umuyese wopatulika; pakuti Ine Yehova wakupatula iwe, ndine woyera,