Leviticus 22:10 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Wapadera asadyeko zinthu zopatulika. Mlendo wongokhala nao kwa wansembe, kapena wantchito wake, asadyeko chinthu chopatulika.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Mlendo asadyeko chopatulikacho; wakungokhala, ndi wansembe, kapena wolembedwa ntchito, asadyeko chopatulikacho.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“ ‘Aliyense amene si wabanja la wansembe, kaya ndi mlendo wa wansembe, kapena wantchito wake, asadye chopereka chopatulika.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Mlendo asadyeko copatulikaco; wakungokhala, ndi wansembe, kapena wolembedwa nchito, asadyeko copatulikaco.