Leviticus 22:12 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mwana wamkazi wa wansembe akakwatiwa ndi wapadera, asadyeko zopereka zopatulikazo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo mwana wamkazi wa wansembe akakwatibwa ndi mlendo, asadyeko nsembe yokweza ya zinthu zopatulika.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mwana wamkazi wa wansembe amene wakwatiwa ndi munthu amene si wansembe, asadyeko nsembe zopatulikazo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo mwana wamkazi wa wansembe akakwatibwa ndi mlendo, asadyeko nsembe yokweza ya zinthu zopatulika.