Leviticus 22:19 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Kuti nsembeyo ilandiridwe, apereke nyama yopanda chilema kaya ndi ng'ombe yamphongo, kapena nkhosa yamphongo kapenanso tonde.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
kuti mulandiridwe, azibwera nayo yaimuna yopanda chilema, ya ng'ombe, kapena nkhosa kapena mbuzi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
ndiye kuti abwere ndi ngʼombe yayimuna, nkhosa yayimuna kapena mbuzi yayimuna. Izi zikhale zopanda chilema kuti zilandiridwe.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
kuti mulandiridwe, azibwera navo yaimuna yopanda cirema, ya ng'ombe, kapena nkhosa, kapena mbuzi.