Leviticus 22:24 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Nyama iliyonse imene mavalo ake ali onyuka kapena otswanyika, kapena ong'ambika kapena oduka, musaipereke ngati nsembe kwa Chauta m'dziko mwanu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Nyama yofula, kapena chopwanya kapena chosansantha, kapena chotudzula, kapena chodula, musamabwera nazo kwa Yehova; inde musamachita ichi m'dziko mwanu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Nyama iliyonse imene mavalo ake ndi onyuka kapena ophwanyika, ongʼambika kapena oduka, musamayipereke kwa Yehova mʼdziko lanu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Nyama yofula, kapena copwanya kapena cosansantha, kapena cotudzula, kapena codula, musamabwera nazo kwa Yehova; inde musamacicita ici m'dziko mwanu.