Leviticus 22:28 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Make akakhala ng'ombe kapena nkhosa, musaphe makeyo pamodzi ndi mwana wake tsiku limodzi.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma musamaipha ng'ombe kapena nkhosa pamodzi ndi mwana wake tsiku limodzimodzi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Musaphe ngʼombe kapena nkhosa pamodzi ndi mwana wake tsiku limodzi. Muyidye pa tsiku lomwelo; musasiyeko ina mpaka mmawa. Ine ndine Yehova.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma musamaipha ng'ombe kapena nkhosa pamodzi ndi mwana wace tsiku limodzimodzi.