Leviticus 22:5 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mwina angathe kukhudza kachilombo kokwaŵa, kamene kangathe kumuipitsa, kapena kukhudza munthu amene angathe kumuipitsa mwa mtundu uliwonse.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
ndi aliyense wokhudza chinthu chokwawa chakudetsedwa nacho, kapenanso munthu amene akamdetsa nacho, chodetsa chake chilichonse;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
kapena kukhudza chilichonse chokwawa chomwe chimadetsa munthu, kapena kukhudza munthu amene angamudetse, kapenanso kukhudza kanthu kena kalikonse kodetsedwa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
ndi ali yense wokhudza cinthu cokwawa cakudetsedwa naco, kapenanso munthu amene akamdetsa naco, codetsa cace ciri conse;