Leviticus 22:6 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Wansembe aliyense wokhudza chinthu chotere, akhala woipitsidwa mpaka madzulo, ndipo asadyeko zinthu zopatulika mpaka atasamba thupi lonse.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
munthu wokhudza chilichonse chotere adzakhala wodetsedwa kufikira madzulo, ndipo asadye zinthu zopatulika, akapanda kusamba thupi lake ndi madzi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Tsono ngati wansembe angakhudze chilichonse mwa zimenezi ndiye kuti adzakhala wodetsedwa mpaka madzulo. Asadye chopereka chilichonse chopatulika mpaka atasamba thupi lake lonse.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
munthu wokhudza ciri conse cotere adzakhala wodetsedwa kufikira madzulo, ndipo asadye zinthu zopatulika, akapanda kusamba thupi lace ndi madzi.