Leviticus 22:9 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Nchifukwa chake ansembe asunge malamulo anga kuti angachimwe ndipo angafe chifukwa choŵaphwanya. Ine ndine Chauta, amene ndimaŵayeretsa.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Potero asunge chilangizo changa, angasenzepo uchimo, ndi kufera m'mwemo, pakuchiipsa; Ine ndine Yehova wakuwapatula iwo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“ ‘Choncho ansembe azisunga malamulo angawa kuti asapezeke wolakwa ndi kufa chifukwa chopeputsa malamulowa. Ine ndine Yehova, amene ndimawayeretsa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Potero asunge cilangizo canga, angasenzepo ucimo, ndi kufera m'mwemo, pakuciipsa; Ine ndine Yehova wakuwapatula iwo,