Leviticus 23:16 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
ndiye kuti masiku asanu mpaka tsiku lotsatana ndi la Sabata lachisanu ndi chiŵiri. Patapita masiku amenewo, mupereke chopereka cha chakudya chatsopano kwa Chauta.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
muwerenge masiku makumi asanu kufikira tsiku lotsata sabata lachisanu ndi chiwiri; pamenepo mubwere nayo kwa Yehova nsembe ya ufa watsopano.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndiye kuti muwerenge masiku makumi asanu kuchokera pa tsiku lotsatana ndi Sabata la chisanu ndi chiwiri, ndipo kenaka mupereke nsembe ya tirigu watsopano kwa Yehova.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
muwerenge masiku makumi asanu kufikira tsiku lotsata sabata lacisanu ndi ciwiri; pamenepo mubwere nayo kwa Yehova nsembe ya ufa watsopano.