Leviticus 23:22 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Pamene mukolola dzinthu m'dziko mwanu, musakolole munda wanu mpaka m'malire mwenimweni, ndipo musatole khunkha lake. Zimenezo musiyire anthu osauka ndiponso alendo. Ine ndine Chauta, Mulungu wanu.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo pakukolola dzinthu za m'dziko mwanu, usamakololetsa m'mphepete mwa munda wako, nusamakunkha khunkha; uzisiyire wosauka ndi mlendo; Ine ndine Yehova Mulungu wako.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“ ‘Pamene mukukolola zinthu mʼmunda mwanu, musakolole munda wanu mpaka mʼmalire mwenimweni, ndipo musatole khunkha lake. Zimenezo musiyire anthu osauka ndi alendo. Ine ndine Yehova Mulungu wanu.’ ”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo pakukolola dzinthu za m'dziko mwanu, usamakololetsa m'mphepete mwa munda wako, nusamakunkha khunkha; uzisiyire wosauka ndi mlendo; Ine ndine Yehova Mulungu wako.