Leviticus 23:25 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Musagwire ntchito zotopetsa, ndipo mupereke nsembe yopsereza kwa Chauta.’ ”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Musamagwira ntchito ya masiku ena; mubwere nayo nsembe yamoto ya Yehova.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Musagwire ntchito zolemetsa koma mupereke nsembe yopsereza kwa Yehova.’ ”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Musamagwira nchito ya masiku ena; mubwere nayo nsembe yamoto ya Yehova.