Leviticus 23:35 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pa tsiku loyamba pazikhala msonkhano wopatulika. Musagwire ntchito zotopetsa.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Tsiku loyamba likhale msonkhano wopatulika, musamagwira ntchito ya masiku ena.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Tsiku loyamba ndi la msonkhano wopatulika, musagwire ntchito zolemetsa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Tsiku loyamba likhale msonkhano wopatulika, musamagwira nchito ya masiku ena.