Leviticus 23:42 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Muzikhala m'misasa masiku asanu ndi aŵiri. Onse amene ali mbadwa m'dziko la Israele azikhala m'misasa,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Mukhale m'misasa masiku asanu ndi awiri; onse obadwa m'dziko mwa Israele akhale m'misasa;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Muzikhala mʼmisasa masiku asanu ndi awiri. Onse amene ali mbadwa mʼdziko la Israeli azikhala mʼmisasa
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Mukhale m'misasa masiku asanu ndi awiri; onse obadwa m'dziko mwa Israyeli akhale m'misasa;