Leviticus 23:43 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
kuti mibadwo yanu idzadziŵe kuti ndine amene ndidakhalitsa Aisraele m'misasa, pamene ndidaŵatulutsa ku dziko la Ejipito. Ine ndine Chauta, Mulungu wanu.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
kuti mibadwo yanu ikadziwe kuti ndinakhalitsa ana a Israele m'misasa, pamene ndinawatulutsa m'dziko la Ejipito; Ine ndine Yehova Mulungu wanu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
kuti zidzukulu zanu zidzadziwe kuti ndine amene ndinakhazika Aisraeli mʼmisasa nditawatulutsa ku Igupto. Ine ndine Yehova Mulungu wanu.’ ”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
kuti mibadwo yanu ikadziwe lruti ndinakhalitsa ana a Israyeli m'misasa, pamene ndinawaturutsa m'dziko la Aigupto; Ine ndine Yehova Mulungu wanu.