Leviticus 25:14 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ukagulitsa mnzako munda, kapena ukagula munda kwa mnzako, pasakhale kuchenjeretsana.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo ukagulitsa kanthu kwa mnansi wako, kapena kugula kanthu ka mnansi wako, musamasautsana;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“ ‘Ngati unagulitsa kapena kugula malo ako kwa mnzako wa mʼdzikomo, pasakhale kuchenjeretsana.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo ukagulitsa kanthu kwa mnansi wako, kapena kugula kanthu ka mnansi wako, musamasautsana;