Leviticus 25:20 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mukafunsa kuti: Kodi pa chaka chachisanu ndi chiŵiri tidzadya chiyani, tikapanda kubzala kapena kukolola dzinthu?
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo mukadzati, Tidzadyanji chaka chachisanu ndi chiwiri? Taonani, sitidzabzala, sitidzakolola dzinthu;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mwina nʼkafunsa kuti, ‘Kodi chaka chachisanu ndi chiwiri tidzadya chiyani ngati sitidzala kapena kukolola mbewu zathu?’
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo mukadzati, Tidzadyanji caka cacisanu ndi ciwiri? taonani, sitidzabzala, sitidzakolola dzinthu;