Leviticus 25:21 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ine ndidzalamula kuti mukhale ndi madalitso pa chaka chachisanu ndi chimodzi, kuti nthaka ibale zakudya zokwanira zaka zitatu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
pamenepo ndidzauza dalitso langa litsike pa inu chaka chachisanu ndi chimodzi, ndipo chidzapatsa zipatso zofikira zaka zitatu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ine ndidzatumiza madalitso ambiri chaka chachisanu ndi chimodzi moti nthaka yanu idzabala zinthu zokwanira kudya zaka zitatu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
pamenepo ndidzauza dalitso langa litsike pa inu caka cacisanu ndi cimodzi, ndipo cidzapatsa zipatso zofikira zaka zitatu.