Leviticus 25:23 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Mtunda usagulitsidwe mpaka muyaya, pakuti dzikolo ndi langa. Inu ndinu alendo ndiponso oyendayenda okhala ndi Ine.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo asaligulitse dziko chigulitsire; popeza dzikoli ndi langa; pakuti inu ndinu alendo akugonera ndi Ine.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“ ‘Malo asagulitsidwe mpaka muyaya chifukwa dzikolo ndi langa. Inu ndinu alendo okhala ndi Ine.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo asaligulitse dziko cigulitsire; popeza dzikoli ndi langa; pakuti inu ndinu alendo akugonera ndi Ine.