Leviticus 25:3 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pa zaka zisanu ndi chimodzi muzikalima minda yanu, ndipo muzikathenera mitengo yanu yamphesa ndi kuthyola zipatso zake.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Zaka zisanu ndi chimodzi ubzale m'munda mwako, ndi zaka zisanu ndi chimodzi udzombole mphesa zako, ndi kucheka zipatso zake;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pa zaka zisanu ndi chimodzi muzikalima minda yanu, ndipo kwa zaka zisanu ndi chimodzi muzikasadza mitengo yanu ya mpesa ndi kuthyola zipatso zake.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Zaka zisanu ndi cimodzi ubzale m'munda mwako, ndi zaka zisanu ndi cimodzi udzombole mphesa zako, ndi kuceka zipatso zace;