Leviticus 25:32 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma kunena za mizinda ya Alevi nyumba zimene zili m'mizinda mwao, Aleviwo angathe kuziwombola nthaŵi iliyonse.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Kunena za midzi ya Alevi, nyumba za m'midzi yaoyao, Alevi akhoza kuziombola nthawi zonse.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“ ‘Alevi ali ndi ufulu owombola nyumba zawo za mʼmidzi yawo nthawi ina iliyonse.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Kunena za midzi ya Alevi, nyumba za m'midzi yao yao, Alevi akhoza kuziombola nthawi zonse.