Leviticus 25:33 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mlevi wina akapanda kuwombola nyumba imene idagulitsidwa mumzinda mwaomoyo aibweze pa chaka chokondwerera zaka 50. Pakuti nyumba zimene zili m'mizinda ya Alevi ndi zao za Aleviwo pakati pa Aisraele.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo munthu akagula kwa Mlevi, nyumba yogulayo yokhala m'mudzi wakewake, ituluke m'chaka choliza lipenga, popeza nyumba za m'midzi ya Alevi ndizo zaozao mwa ana a Israele.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma ngati Mlevi sawombola nyumba imene inagulitsidwa mʼmudzi mwake, ndiye kuti idzabwezedwe mʼchaka choliza lipenga pokondwerera zaka makumi asanu, popeza nyumba zimenezi zili mʼmidzi ya Alevi ndi yawo pakati pa Aisraeli.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo munthu akagula kwa Mlevi, nyumba yogulayo yokhala m'mudzi wace wace, ituruke m'caka coliza lipenga, popeza nyumba za m'midzi ya Alevi ndizo zao zao mwa ana a Israyeli.