Leviticus 25:38 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ine ndine Chauta, Mulungu wanu, amene ndidakutulutsani m'dziko la Ejipito kuti ndikupatseni dziko la Kanani, ndipo kuti ndikhale Mulungu wanu.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ine ndine Yehova Mulungu wanu, amene ndinakutulutsani m'dziko la Ejipito, kukupatsani dziko la Kanani, kuti ndikhale Mulungu wanu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ine ndine Yehova Mulungu wanu, amene ndinakutulutsani mʼdziko la Igupto kuti ndikupatseni dziko la Kanaani ndi kuti ndikhale Mulungu wanu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ine ndine Yehova Mulungu wanu, amene ndinakuturutsani m'dziko la Aigupto, kukupatsani dziko la Kanani, kuti ndikhale Mulungu wanu.