Leviticus 25:39 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Mbale wako amene ukukhala naye akakhala wosauka nadzigulitsa kwa iwe, usamuyese kapolo wako.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo mbale wako akasaukira chuma, ndi kudzigulitsa kwa iwe; usamamgwiritsa ntchito monga kapolo;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“ ‘Ngati mʼbale wanu asauka ndipo adzigulitsa yekha kwa inu, musamugwiritse ntchito ngati kapolo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo mbale wako akasaukira cuma, ndi kudzigulitsa kwa iwe; usamamgwiritsa nchito monga kapolo;