Leviticus 25:40 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Akhale ngati wantchito wako, ndiponso ngati mlendo wako. Azikugwirira ntchito mpaka chaka chokondwerera zaka 50.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
azikhala nawe ngati wolipidwa ntchito, ngati mlendo wako; akutumikire kufikira chaka choliza lipenga.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Akhale ngati wantchito kapena ngati mlendo. Akugwirireni ntchito mpaka chaka chokondwerera zaka makumi asanu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
azikhala nawe ngati wolipidwa nchito, ngati munthu wokhala nawe; akutumikire kufikira caka coliza lipenga.