Leviticus 25:42 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Aisraele ndi atumiki anga amene ndidaŵatulutsa ku dziko la Ejipito, asagulitsidwe ngati akapolo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pakuti iwo ndiwo atumiki anga, amene ndinawatulutsa m'dziko la Ejipito; asamawagulitsa monga amagulitsa kapolo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Chifukwa Aisraeli ndi atumiki anga amene ndinawatulutsa mʼdziko la Igupto, asagulitsidwe ngati akapolo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakuti iwo ndiwo atumiki anga, amene ndinawaturutsa m'dziko la Aigupto; asamawagulitsa monga amagulitsa kapolo.