Leviticus 25:44 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Kunena za akapolo aamuna kapena aakazi oti muzikhala nawo, mungathe kuŵagula kwa mitundu ina ya anthu okuzungulirani.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Kunena za kapolo wako wamwamuna, kapena wamkazi amene ukhala nao; azikhala a amitundu akuzungulira inu, kwa iwowa muzigula akapolo aamuna ndi aakazi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“ ‘Kunena za akapolo aamuna ndi aakazi, amenewa mungathe kuwagula kuchokera kwa mitundu ya anthu imene yakuzungulirani.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Kunena za kapolo wako wamwamuna, kapena wamkazi amene ukhala nao; azikhala a amitundu akuzungulira inu, kwa iwowa muzigula akapolo amuna ndi akazi.