Leviticus 25:45 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mungathenso kuŵagula pakati pa alendo amene akukhala pakati panu ndiponso pakati pa mabanja okhala nanu amene adabadwira m'dziko mwanu. Amenewo angathe kukhala anu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Muwagulenso ana a alendo akukhala mwa inu, a iwowa ndi a mabanja ao akukhala nanu, amene anabadwa m'dziko lanu; ndipo adzakhala anuanu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mungathenso kugula akapolo kuchokera kwa alendo amene akukhala nanu kapena kuchokera ku mabanja amene mukukhala nawo amene ndi mbadwa za mʼdziko lanu. Iwowa akhoza kukhala akapolo anu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Muwagulenso ana a alendo akukhala mwa inu, a iwowa ndi a mabanja ao akukhala nanu, amene anabadwa m'dziko lanu; ndipo adzakhala anu anu.