Leviticus 25:47 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Mlendo kapena munthu wodzangokhala nanu akalemera, ndipo mbale wanu wokhala naye pafupi akakhala wosauka, nadzigulitsa yekha kwa mlendoyo kapena kwa munthu wodzangokhala nanu uja, kapena kwa aliyense wa banja la mlendolo,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo mlendo wakugonera kwanu akalemera chuma, ndi mbale wako wakukhala naye akasauka, nadzigulitsa kwa mlendo wakugonera kwanu, kapena kwa fuko la banja la mlendo;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“ ‘Ngati mlendo kapena munthu amene akukhala nanu kwa kanthawi kochepa alemera ndipo mmodzi wa abale anu amene akukhala naye pafupi nʼkusauka, nadzigulitsa yekha kwa mlendo amene akukhala pakati panuyo kapena kwa mmodzi wa fuko la munthu wongokhala pafupi nayeyo,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo mlendo wakugonera kwanu akalemera cuma, ndi mbale wako wakukhala naye akasauka, nadzigulitsa kwa mlendo wakugonera kwanu, kapena kwa pfuko la banja la mlendo;