Leviticus 25:49 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
kapena mbale wa bambo wake, kapena mwana wa mbale wa bambo wake, kapena wachibale wa pabanja pake, onseŵa angathe kumuwombola. Koma wodzigulitsayo akalemera, angathe kudziwombola yekha.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
kapena mbale wa atate wake, kapena mwana wa mbale wa atate wake amuombole, kapena mbale wake aliyense wa banja lake amuombole; kapena akalemera chuma yekha adziombole yekha.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
amalume ake kapena mwana wa amalume ake, kapena wachibale wa mu fuko lake. Kapena ngati iye mwini alemera, atha kudziwombola yekha.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
kapena mbale wa atate wace, kapena mwana wa mbale wa atate wace amuombole, kapena mbale wace ali yense wa banja lace amuombole; kapena akalemera cuma yekha adziombole yekha.