Leviticus 25:51 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Zaka zikakhala kuti zikadalipo zambiri, pa mtengo umene adalipira pomgula, iye abweze mtengo womuwombolerawo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Zikamtsalira zaka zambiri, monga mwa izi abwezere ndalama zakumuombola zochokera ku ndalama zomgulazo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ngati patsala zaka zambiri, iye ayenera kulipira mtengo woposera umene anamugulira.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Zikamtsalira zaka zambiri, monga mwa izi abwezere ndarama zakumuombola zocokera ku ndalama zomgulazo.