Leviticus 25:53 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Azikhala naye ngati wantchito wolembedwa, chaka ndi chaka. Asamlamule mwankhalwe, iwe ukupenya.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Akhale naye monga wolipidwa chaka ndi chaka; asamamlamulira momzunza pamaso pako.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Azikhala naye ngati wantchito wolembedwa chaka ndi chaka. Ndipo muonetsetse kuti mbuye wakeyo sakumulamulira mwankhanza.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Akhale naye monga wolipidwa caka ndi caka; asamamlamulira momzunza pamaso pako,