Leviticus 25:6 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Chaka chachisanu ndi chiŵiri chopumulacho chidzakupatsani chakudya chokwanira nonsenu, inuyo ndi akapolo anu aamuna ndi aakazi, antchito anu pamodzi ndi alendo amene akukhala nanu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Sabata la dzikoli likhale kwa inu la chakudya; kwa iwe, ndi mnyamata wako, ndi mdzakazi wako, ndi wolembedwa ntchito yako, ndi mlendo wako wakugonera kwanu;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Chaka chimene nthakayo ipumula mudzakhala ndi chakudya chokwanira inuyo, akapolo anu aamuna ndi aakazi, antchito ndi alendo okhala nanu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo sabata la dzikoli likhale kwa inu la cakudya; kwa iwe, ndi mnyamata wako, ndi mdzakazi wako, ndi wolembedwa nchito yako, ndi mlendo wako wakugonera kwanu;