Leviticus 26:10 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Muzidzadyabe sundwe wakalekale, koma mudzachotsa sundweyo m'khokwe, kuti zatsopano zipeze malo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo mudzadya za sundwe wakale ndi kutulutsa zakale chifukwa cha zatsopano.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mudzakhala mukudyabe chakudya chogonera ndipo mudzachotse chakudyacho mʼnkhokwe kuti mupezemo malo woyika chakudya china chatsopano.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo mudzadya za sundwe wakale ndi kuturutsa zakale cifukwa ca zatsopano.