Leviticus 26:11 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndidzakhala pakati panu ndipo sindidzaipidwa nanu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndidzamanga Kachisi wanga pakati pa inu, ndipo moyo wanga sudzanyansidwa nanu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndidzakhala pakati panu, ndipo sindidzayipidwa nanu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndidzamanga kacisi wanga pakati pa inu, ndipo moyo wanga sudzanyansidwa nanu.