Leviticus 26:18 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mukapanda kundimvera mutaona zonsezi, ndidzakulanganinso mochulukitsa kasanunkaŵiri chifukwa cha machimo anu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo mukapanda kundimvera, zingakhale izi, ndidzaonjeza kukulangani kasanu ndi kawiri chifukwa cha zochimwa zanu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“ ‘Ngati simudzandimvera mutaona zonsezi, ndidzakulanganinso mochulukitsa kasanu ndi kawiri chifukwa cha kuchimwa kwanu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo muka panda kundimvera, zingakhale izi ndidzaonjeza kukulangani kasanu nd kawiri cifukwa ca zocimwa zanu.