Leviticus 26:20 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Nyonga zanu zidzapita pachabe, poti nthaka yanu sidzabala kanthu, ndipo mitengo yake sidzabala zipatso.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
ndipo mudzachita nayo mphamvu yanu chabe; ndi nthaka yanu siidzapereka zipatso zake, ndi mitengo ya m'dziko siidzabala zobala zake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mphamvu zanu zidzapita pachabe chifukwa nthaka yanu sidzabala kanthu, ngakhale mitengo yake sidzabala zipatso zake.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
ndipo mudzacita nayo mphamvu yanu cabe; ndi nthaka yanu siidzapereka zipatse zace, ndi mitengo ya m'dziko siidzabala zobala zace.