Leviticus 26:21 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Tsono mukamayenda motsutsana ndi Ine osandimvera, ndidzabweretsa miliri inanso pa inu, yopambana machimo anu kasanunkaŵiri.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo mukayenda motsutsana nane, osalola kumvera Ine; ndidzakuonjezerani miliri kasanu ndi kawiri, monga mwa zochimwa zanu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“ ‘Ngati mudzapitirira kutsutsana nane ndi kukana kundimvera, ndidzachulukitsa masautso anu kasanu ndi kawiri molingana ndi machimo anu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo mukayenda motsutsana nane, osalola kumvera Ine; ndidzakuonjezerani miliri kasanu ndi kawiri, monga mwa zocimwa zanu.