Leviticus 26:28 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Inenso ndidzalimbana nanu mwaukali, ndipo Ine mwiniwake ndidzakulangani mochulukitsa kasanunkaŵiri chifukwa cha machimo anu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ine ndidzayenda nanu motsutsana mwa kukuzazirani, ndi kukulangani Inedi kasanu ndi kawiri chifukwa cha zochimwa zanu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
pamenepo ndidzalimbana nanu mwaukali, ndipo Ine mwini ndidzakulangani mochulukitsa kasanu ndi kawiri chifukwa cha kuchimwa kwanu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ine ndidzayenda nanu motsutsana mwa kukuzazirani, ndi kukulangani Inedi kasanu ndi kawiri cifukwa ca zocimwa zanu.