Leviticus 26:41 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Paja chifukwa cha zimenezo Ine ndidatsutsana nawo ndi kuŵafikitsa ku dziko la adani ao. Tsono mitima yao youma idzadzichepetsa ndi kulola kulangidwa chifukwa cha machimo ao.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Inenso ndinayenda motsutsana nao, ndi kuwatengera ku dziko la adani ao. Ngati tsono mtima wao wosadulidwa udzichepetsa, ndipo avomereza kulanga kwa mphulupulu zao;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
zomwe zinandipangitsa kuwafulatira ndi kuwapereka mʼmanja mwa adani awo. Ndipo mitima yawo yowumayo ikadzadzichepetsa ndi kuvomera kulangidwa chifukwa cha machimo awo,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Inenso ndinayenda motsutsana nao, ndi kuwatengera ku dziko la adani ao. Ngati tsono mtima wao wosadulidwa udzicepetsa, ndipo abvomereza kulanga kwa mphulupulu zao;