Leviticus 27:11 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ikakhala nyama yonyansa, yonga imene siloledwa kuipereka ngati nsembe kwa Chauta, munthuyo abwere ndi nyamayo kwa wansembe.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo chikakhala cha nyama yodetsa, imene sabwera nayo ikhale chopereka cha Yehova, aike nyamayi pamaso pa wansembe;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ngati chimene anachitira lumbiro ndi nyama yodetsedwa, nyama imene siloledwa kuyipereka kukhala nsembe kwa Yehova, nyamayo abwere nayo kwa wansembe,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo cikakhala ca nyama yodetsa, imene sabwera nayo ikhale copereka ca Yehova, aike nyamayi pamaso pa wansembe;