Leviticus 27:12 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndipo wansembe atchule mtengo wake poona ngati njabwino kapena ai. Monga momwe iwe wansembe utchulire, mtengo udzakhala momwemo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
ndipo wansembeyo aiyese mtengo wake, ingakhale yokoma kapena yoipa; monga uiyesa wansembewe, momwemo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
ndipo wansembeyo atchule mtengo wake poona ngati ndi yabwino kapena ndi yoyipa. Mtengo umene wansembe atchule ndiwo udzakhale mtengo wake.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
ndipo wansembeyo aiyese mtengo wace, ingakhale yokoma kapena yoipa; monga uiyesa wansembewe, momwemo.