Leviticus 27:13 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma akafuna kuti aiwombole, aonjezepo pa mtengo wake wa nyamayo chimodzi mwa zigawo zisanu za mtengo wakewo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo akaiombola ndithu, pamenepo aonjezepo limodzi la magawo asanu la mtengo wake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ngati mwini wakeyo akufuna kuwombola nyamayo, awonjezere pa mtengo wake wa nyamayo chimodzi mwa zigawo zisanu zamtengowo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo akaiombola ndithu, pamenepo aonjezepo limodzi la magawo asanu la mtengo wace.